Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g05 3/8 tsamba 1-2
  • Zamkatimu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zamkatimu
  • Galamukani!—2005
  • Nkhani Yofanana
  • Zimene Muyenera Kudziwa Zokhudza Magetsi ndi Mafuta
    Galamukani!—2017
  • Kupeza Gwero la Mphamvu Zonse
    Galamukani!—2005
  • Mafuta—Kodi Adzatha?
    Galamukani!—2003
  • N’chifukwa Chiyani Mphamvu za Magetsi Zili Zofunika Kwambiri pa Moyo Wathu?
    Galamukani!—2005
Onani Zambiri
Galamukani!—2005
g05 3/8 tsamba 1-2

Zamkatimu

March 8, 2005

Kodi Tingathe Kupanga Magetsi Popanda Kuwononga Chilengedwe?

Popeza panopa magetsi amene anthu amagwiritsa ntchito akuchulukirachulukira, kodi m’tsogolo muno padzakhala magetsi okwanira aliyense? Kodi pali njira zina zopangira magetsi popanda kuwononga chilengedwe m’malo mwa mafuta, malasha, gasi, ndi maatomu? Nkhani za m’magazini ino zikuyankha mafunso amenewa.

3 N’chifukwa Chiyani Mphamvu za Magetsi Zili Zofunika Kwambiri pa Moyo Wathu?

4 N’chifukwa Chiyani Tikufunika Njira Zatsopano Zopangira Magetsi?

7 Kodi Pali Njira Zatsopano Zotani Zopangira Magetsi?

10 Kupeza Gwero la Mphamvu Zonse

11 Mavuto Amene Amayi Amakumana Nawo

13 Amayi Akuthana ndi Mavutowa

17 Ntchito Yolemekezeka ya Amayi

20 Zimene Baibulo Limanena

Kodi Mulungu Ali Paliponse?

22 Tomato Amagwira Ntchito Zambiri

18 Achinyamata Akufunsa Kuti . . .

Kodi Ndingatani Kuti Ndiziugwira Mtima?

31 ‘Magazini Yochokera kwa Mulungu’

32 Mukuitanidwa ku Msonkhano Wofunika Kwambiri pa Chaka

Ndine Wokonzeka Kuthandiza Ena 24

Werengani za momwe mtsikana ameneyu anaphunzitsira anthu a m’banja mwake choonadi cha m’Baibulo, omwe amakhala ku Madagascar kutali kwambiri ndi tauni.

[Chithunzi patsamba 2]

DZUWA

[Chithunzi patsamba 2]

MPHEPO

[Chithunzi patsamba 2]

MADZI OTENTHA A PANSI PA NTHAKA

[Mawu a Chithunzi]

DOE Photo

[Chithunzi patsamba 2]

MADZI

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena