Zamkatimu
April 8, 2005
Kuthandiza Achinyamata Amene Ali Pamavuto
Akatswiri ambiri akunena kuti achinyamata a masiku ano ali ndi mavuto ambiri. Nkhani za m’magazini ino zikufotokoza zifukwa zina zimene zikuchititsa achinyamata kukhala pamavuto ndiponso zili ndi malangizo othandiza achinyamata ndi makolo.
3 Zinthu Sizikuwayendera Bwino Achinyamata
5 Mavuto Amene Achinyamata Akukumana Nawo Masiku Ano
9 Zimene Zingathandize Achinyamata Masiku Ano
12 Kodi Mumayendetsa Galimoto Mbali Iti ya Msewu?
19 N’chifukwa Chiyani Mapiri Ali Ofunika kwa Ife?
27 Kodi Ndani Adzapulumutse Mapiri?
31 Kodi Akaidi Angatheke Kuwasintha?”
32 Mayankho Othandiza a Mafunso Amene Mwakhala Mukufunsa
Kodi Mulungu Amavomereza Maukwati a Amuna Okhaokha Kapena Akazi Okhaokha? 16
Nkhani imeneyi yabutsa mkangano waukulu. Kodi Baibulo limapereka malangizo omveka bwino otani pa nkhani imeneyi?
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photo by Chris Hondros/Getty Images