Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • g 7/06 tsamba 13-31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
  • Galamukani!—2006
  • Timitu
  • Nkhani Yofanana
  • KODI ZINACHITIKIRA KUTI?
  • ZINACHITIKA LITI?
  • NDINE NDANI?
  • NDINE NDANI?
  • KUCHOKERA M’MAGAZINI INO
  • Zithunzi Zoti Ana Apeze
  • MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2006
  • Kodi Mungayankhe Bwanji?
    Galamukani!—2007
Onani Zambiri
Galamukani!—2006
g 7/06 tsamba 13-31

Kodi Mungayankhe Bwanji?

KODI ZINACHITIKIRA KUTI?

1. Kodi izi zinachitikira mu mzinda uti?

Lembani mzere kuzungulira yankho lanu pa mapupa.

Tariso

Antiokeya (wa ku Suriya)

Damasiko

Yerusalemu

◆ Kodi ndani amene ali m’basiketiyu?

․․․․․

◆ N’chifukwa chiyani akuthawa mu mzindawu?

․․․․․

◼ Kambiranani: Kodi ndi liti pamene mungathawe mavuto? Kodi Akristu amafunikira kuthawa mavuto nthawi zonse? N’chifukwa chiyani mukuyankha choncho?

ZINACHITIKA LITI?

Lembani mzere kuchokera pa chithunzi kufika pa chaka cholondola.

1513 B.C.E. 1512 1473 1450 468 455

2. Yoswa 24:1-25

3. Eksodo 32:1-6, 19

4. Ezara 8:1, 21, 31

NDINE NDANI?

5. Ndinkasoka zovala; mayina anga onse awiri amatanthauza “Mphoyo,” ndipo ndinaukitsidwa kwa akufa.

NDINE NDANI?

6. Ndinkakhala m’mphepete mwa nyanja ndipo nthawi ina ndinalandira mlendo wotchuka yemwe ankakonda kusodza. Tonse awiri tili ndi mayina ofanana.

KUCHOKERA M’MAGAZINI INO

Yankhani mafunso awa, ndipo lembani vesi kapena mavesi a m’Baibulo lomwe likusowapo.

Tsamba 8 Kodi mwamuna ayenera kukhala motani ndi mkazi wake? (Akolose 3:․․․)

Tsamba 8 Kodi njira yabwino yothetsera mavuto m’banja n’njotani? (1 Petro 4:․․․)

Tsamba 15 Kodi Mulungu amakhala pa malo enaake? (1 Mafumu 8:․․․)

Tsamba 25 Kodi n’kuti kumene mungapeze malangizo abwino okhudza ntchito yomwe mukufuna kugwira? (Miyambo 3:․․․)

Zithunzi Zoti Ana Apeze

Kodi mungathe kupeza zithunzi izi m’magazini ino? M’mawu anuanu, fotokozani zimene zikuchitika pa chithunzi chilichonse.

(Mayankho ali patsamba 13)

MAYANKHO A MAFUNSO A PA TSAMBA 31

1. Damasiko.—Machitidwe 9:19, 25.

◆ Saulo, yemwe anadzatchedwa Paulo.—Machitidwe 9:17-19.

◆ Ayuda ankafuna kumupha chifukwa choti ankachitira umboni.—Machitidwe 9:22-24.

2. 1450 B.C.E.

3. 1513 B.C.E.

4. 468 B.C.E.

5. Tabita, kapena Dorika.—Machitidwe 9:36-41.

6. Simoni wofufuta zikopa.—Machitidwe 10:5, 6.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena