Zamkatimu
September 2007
Kodi Mulungu Ndiye Amachititsa Masoka Achilengedwe?
Anthu ambiri amaganiza kuti Mulungu ndiye amachititsa zivomezi, nyengo yoipa kwambiri, ndiponso masoka ena achilengedwe. Komatu Baibulo limafotokoza zinthu zosiyana ndi zimenezi.
3 N’zothetsa Nzeru Ndiponso Zowononga Chikhulupiriro
4 Kodi Mulungu Ndiye Amawachititsa?
12 Nyumba Zobatiziramo Anthu Umboni wa Mwambo Woiwalika
23 Tizakudya Tokoma Tam’tchire
26 Munthu Wosangalala Kodi Amakhaladi ndi Thanzi Labwino?
27 Mano Akhala Akuvutitsa Anthu Kuyambira Kalekale
30 “Athandiza Kwambiri Pazachipatala”
32 “Zingakhale Bwino Aliyense Atawerenga Buku Limeneli”
Kodi N’kulakwa Kugwiritsira Ntchito Njira za Kulera? 10
Kodi Baibulo lili ndi malangizo alionse omwe mwamuna ndi mkazi wake angatsatire pa nkhani ya kulera?
Kodi Nditsatire Chikhalidwe Chiti? 18
Kodi ndi mavuto otani amene achinyamata amakumana nawo banja lawo likasamukira ku dziko lina?