Zamkatimu
March 2009
Kodi Ndinu Kapolo wa Ndalama?
Ndalama zimathandiza kwambiri. Koma kodi n’chifukwa chiyani anthu ambiri amakhala ndi nkhawa zokhudza ndalama? Werengani za mmene mungaonere ndi kugwiritsira ntchito ndalama mwanzeru.
3 Kodi Ndinu Kapolo wa Ndalama?
5 Muzigwiritsa Ntchito Ndalama Mwanzeru
12 Tinadalitsidwa Chifukwa Chokonda Kwambiri Mulungu
21 Mphunzitsi Anasintha Maganizo Ake
24 Kachipangizo Kochititsa Chidwi
32 Tsiku Loyenera Kulikumbukira
Kodi Kutentha Mtembo N’kulakwa? 10
Kodi pali chilichonse cholakwika ndi kutentha mtembo?
Kodi Mungatani Kuti Mwana Wanu Asanenepe Kwambiri? 27
N’chiyani chikuchititsa kuti padziko lonse ana azinenepa kwambiri? Kodi mungawathandize bwanji ana anu kuti asanenepe kwambiri?