Zamkatimu
April 2010
Kodi Nthawi Imakucheperani?
Pafupifupi tonsefe nthawi imatichepera ndipo timalephera kumaliza ntchito zimene tinakonza kuti tichite. Koma kodi tingatani kuti tisamapanikizike kwambiri?
4 Kodi Mungatani Kuti Muzigwiritsa Ntchito Nthawi Mwanzeru?
7 Mfundo 20 Zothandizani Kuti Muzikhala ndi Nthawi Yokwanira
9 Muzikhala ndi Nthawi Yochita Zinthu Zofunika Kwambiri?
13 Zimene Anyani Amachita Akakhala M’tchire
16 M’nkhalango ya Amazon Muli Zamoyo Zambiri
22 Mont Blanc—Phiri Lalitali Kwambiri ku Ulaya
32 Kodi Mulungu Amatisamaliradi?
Ndinasankha Ntchito Yabwino 10
Nthawi zina ndibwino kudzifufuza kuti tione ngati tikugwiritsa ntchito moyo wathu mwanzeru. Werengani nkhaniyi kuti muone mmene katswiri wina wazojambulajambula ku Bulgaria anachitira zimenezi.
Kodi Kugonana Tili Pachibwenzi Kungachititse Kuti Tizikondana Kwambiri? 26
Baibulo limanena kuti munthu amene amachita dama amakhala akuchimwira thupi lake. Kodi zimenezi n’zoona?