Zamkatimu
June 2010
Zimene Mungachite Ngati Mumapanikizika Kwambiri
Akuti kupanikizika n’koopsa kwambiri kuposa chinthu china chilichonse pa moyo wathu. Werengani nkhanizi kuti mudziwe zimene thupi lathu limachita tikapanikizika, ndiponso zimene tingachite kuti tisamapanikizike kwambiri.
3 Kupanikizika N’koopsa Kwambiri
4 Kupanikizika Kumayambitsa Mavuto Aakulu
6 Zimene Tingachite Kuti Tisamapanikizike Kwambiri
10 Mbalame Zampala Zimene Zinaletsedwa Kuulukira Kutali
16 Njanji Yochoka Kunyanja Kukafikanso Kunyanja
27 Tetezani Banja Lanu ku Matenda a Chimfine
32 “ Khalanibe pa Ubwenzi ndi Yehova”
Matenda Ofooketsa Mafupa Amayamba Mosaonekera 19
M’mayiko a ku Ulaya, pa masekondi 30 alionse, munthu mmodzi amathyoka fupa chifukwa cha matenda ofooketsa mafupa. Ku United States, akuti mkazi mmodzi pa akazi awiri alionse a zaka zoposa 50, akhoza kudzathyoka fupa pa nthawi inayake pa moyo wake chifukwa cha matendawa. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene mungachite kuti mupewe matendawa.
Ndinasiya Ntchito ya Ndalama Zambiri 24
Martha anatchuka ndiponso analemera chifukwa cha ntchito yoimba koma kenako anasiya. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene zinachititsa kuti asiye ntchitoyi komanso zimene zinamuthandiza kuti akhale wosangalala.