Zamkatimu
November 2010
Anthu Okhulupirira Kuti Kulibe Mulungu Ali Pa Kampeni
Ena mwa anthu otchuka kwambiri padzikoli amene amakhulupirira zoti kulibe Mulungu ali pa kampeni. Cholinga chawo n’chakuti anthu enanso ngati inuyo muyambe kukhulupirira zomwezo. Koma kodi mfundo zawo n’zomveka?
3 Anthu Okhulupirira Kuti Kulibe Mulungu Ali pa Kampeni
4 Kodi Pali Umboni Wasayansi Wotsimikizira Zoti Kulibe Mulungu?
6 Kodi Zinthu Zingayambe Kuyenda Bwino Padzikoli Patakhala Kuti Palibe Zipembedzo?
8 “ Ndinakulira M’banja Losakhulupirira Kuti Kuli Mulungu”
10 Zimene Amachita ku Mumbai Kuti Azidya Chakudya Chotentha Kuntchito
19 Malangizo Omwe Angatithandize Kulamulira Lilime Lathu
22 Makadamiya—Mtedza Wokoma wa ku Australia
32 Kodi N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudziwa Uthenga wa M’Baibulo?
Buku Limene Mungathe Kulikhulupirira—Gawo 1 15
Nkhaniyi ndi yoyamba pa nkhani 7 zotsatizana zimene zizifotokoza mbiri ndi ulosi wa m’Baibulo. Cholinga cha nkhanizi ndi kukuthandizani kuona kuti Baibulo ndi lolondola komanso lodalirika.
Kodi muyenera kusiyira pati sukulu? Kodi zolinga zanu pa nkhani ya maphunziro ndi zotani? Nkhaniyi ikuthandizani kusankha zinthu mwanzeru.
[Mawu a Chithunzi patsamba 2]
Photograph taken by courtesy of the British Museum