Zamkatimu
October 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
NKHANI
Nkhaniyi ili ndi mfundo zimene zingakuthandizeni kuti muzikhulupirira zoti Mulungu ndi amene analenga zonse.
Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zifukwa ziwiri zimene zingakuthandizeni kudziwa ngati zilidi zoona kuti zamoyo zinachita kusintha kuchokera ku zinthu zina.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ACHINYAMATA)
MAVIDIYO
Vidiyoyi ikusonyeza Kalebe ali ndi bambo ake ndipo akuona zinthu zimene Yehova analenga.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)