Zamkatimu
November 2015
© 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
7 Amachita Zinthu Bwinobwino Ngakhale Kuti Ndi Osaona
MUNGAPEZENSO ZINTHU ZOTSATIRAZI PA WEBUSAITI YATHU
NKHANI
Zokhudza Ifeyo
Werengani nkhani imene ingakuthandizeni kudziwa ngati n’zoona kuti a Mboni za Yehova amakhulupirira zoti iwo okha ndi amene adzapulumuke.
Mungapezenso mayankho a mafunso ambiri amene mungakhale nawo monga:
Kodi a Mboni za Yehova ndi Akhristu?
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZOKHUDZA IFEYO > MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI)
MAVIDIYO
Ana
Onerani mavidiyo osangalatsa a ana, mwachitsanzo vidiyo yomwe ingakuthandizeni kuti muzikhululuka ndi mtima wonse.
(Pitani pomwe palembedwa kuti ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA > ANA)