Mawu Oyamba
Masiku ano pali matenda ambiri oopsa. Koma kodi tingadziteteze bwanji?
Baibulo limanena kuti: “Wochenjera ndi amene amati akaona tsoka amabisala.”—Miyambo 22:3.
“Galamukani!” iyi ikufotokoza zimene tingachite kuti tidziteteze ku matenda.