Nyimbo 83
Chifukwa cha Kukondwera cha Ziyoni
1. M’lungu ali ndi mtundu;
Wobadwatu lero.
“Dziko” linakhalapo
Sitidzaliranso.
Ziyoni wakumwamba—
Anabala ana
A’muna amenetu
Adziŵitsa M’lungu.
(Korasi)
2. Kubadwa kwa mtunduwu
Kwadzetsa chimwemwe.
Usamalira zinthu
Ndi nkhosa za M’lungu.
E, ana a Ziyoni
Awopa mawuwo.
Alalika molimba.
Samawopa chinthu.
(Korasi)
3. Chiri chifuno cha
Ya Mitundu iwope.
Mitundu yosankhidwa
Imka ku Ziyoni.
Ndimwaŵi wa padera
Kukwezetsa mbiri,
Ndi kumulambiradi,
Atchula dzinalo.
(KORASi)
Kodwerani ndi Ziyoni mmwamba!
Chikondi cha Ya nchachikuludi!
Ana padziko atumikira,
pagomelo la Ya aseyama.