Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ssb nyimbo 210
  • ‘Tsimikizirani Zinthu Zofunika Kopambana’

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Tsimikizirani Zinthu Zofunika Kopambana’
  • Imbirani Yehova Zitamando
  • Nkhani Yofanana
  • Chikondi Chanu Chipitirire Kukula
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2019
  • “Muzitsimikizira Kuti Zinthu Zofunika Kwambiri Ndi Ziti”
    Imbirani Yehova
  • Yesetsani Kukhala Ngati Wamng’ono
    Nsanja ya Olonda—2012
  • Kulani M’chikondi
    Nsanja ya Olonda—2001
Onani Zambiri
Imbirani Yehova Zitamando
Ssb nyimbo 210

Nyimbo 210

‘Tsimikizirani Zinthu Zofunika Kopambana’

(Afilipi 1:10)

1. Titumikira Ya Mulungu timamukonda.

Chikondi ndi chofunika; chichoka kumwamba.

Chikondi cho chikuletu potsimikiza

Za zinthu zolungamazo.

Tisalakwetu tichite zambiri muntchito ya Ya.

2. Zinthu zofunika ndi Mulungu tiyamika,

Mveranitu mokondwa ndi kusunga umphumphu.

Ndi onsewo mumtendere mukhale nawo

Osakhumudwitsa koma

—Muwauze za chiyembekezo ndi kuthandizana.

3. Nkofunika kukometsera chiphunzitsocho,

Tikadzichepetsa sitidzakana uphungu.

Tidzazidwe chilungamo, mbiri yabwino

Muntchito yotamanda Ya.

Motero tidzatsimikizira zinthu zofunika.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena