Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • bt tsamba 100
  • “Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”
  • ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
  • Nkhani Yofanana
  • “Mpingo Umene Unali ku Yerusalemu Unayamba Kuzunzidwa Koopsa”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
  • Mmene Zinthu Zimayendetsedwera mu Mpingo
    Gulu Lochita Chifuniro cha Mulungu
  • Mawu a Mulungu Amatithandiza Kuti Tizichita Zinthu Mwadongosolo
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • “Anatumizidwa ndi Mzimu Woyera”
    ‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
Onani Zambiri
‘Kuchitira Umboni Mokwanira za Ufumu wa Mulungu’
bt tsamba 100
Sila ndi Yudasi akuwerengera mpingo wa ku Antiokeya wa ku Siriya mpukutu.

GAWO 5 • MACHITIDWE 15:1-35

“Atumwi ndi Akulu Anasonkhana”

MACHITIDWE 15:6

Mumpingo munayambika nkhani yovuta imene ikanasokoneza mtendere komanso mgwirizano wa Akhristu. Kodi malangizo othetsera nkhani imeneyi anachokera kuti? M’gawoli, tiona mmene mpingo wa m’nthawi ya atumwi unkayendera, ndipo anthu a Mulungu masiku ano amatsanzira chitsanzo chimenechi.

Woyang’anira dera akukamba nkhani pa mpingo.
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena