Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rr tsamba 73
  • Mitundu Imene Inazungulira Yerusalemu

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mitundu Imene Inazungulira Yerusalemu
  • Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Nkhani Yofanana
  • Ulosi Wonena za Kuwonongedwa kwa Turo Umatithandiza Kuti Tizikhulupirira Kwambiri Mawu a Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2017
  • Anthu a Mitundu Ina “Adzadziwa kuti Ine Ndine Yehova”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Kodi Mukudziwa?
    Nsanja ya Olonda—2008
  • Maulosi Amene Anakwaniritsidwa
    Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu?
Onani Zambiri
Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
rr tsamba 73

BOKOSI 7A

Mitundu Imene Inazungulira Yerusalemu

cha m’ma 650-300 B.C.E.

Losindikizidwa

TCHATI CHOSONYEZA NTHAWI (ZAKA ZONSE NDI ZA MU B.C.E.)

  1. 620: Ababulo anayamba kulamulira Yerusalemu

    Nebukadinezara anachititsa kuti mfumu ya ku Yerusalemu ikhale pansi pa ulamuliro wake

  2. 617: Ababulo anatenga gulu loyamba la akapolo kuchokera ku Yerusalemu

    Anatenga olamulira, asilikali amphamvu ndi amisiri n’kupita nawo ku Babulo

  3. 607: Ababulo anawononga Yerusalemu

    Mzindawo ndi kachisi wake zinawotchedwa

  4. Pambuyo pa 607: Mzinda wa Turo wakumtunda

    Nebukadinezara anaukira mzinda wa Turo kwa zaka 13. Iye anagonjetsa mzinda wa Turo wakumtunda koma mzinda wa Turo wapachilumba anausiya

  5. 602: Aamoni ndi Amowabu

    Nebukadinezara anaukira Aamoni ndi Amowabu

  6. 588: Ababulo anagonjetsa Aiguputo

    M’chaka cha 37 cha ulamuliro wake, Nebukadinezara anaukira Aiguputo

  7. 332: Mzinda wa Turo wapachilumba

    Gulu lankhondo la Agiriki limene ankalitsogolera ndi Alekizanda Wamkulu, linawononga mzinda wa Turo wapachilumba

  8. 332 kapena chakachi chisanafike: Filisitiya

    Alekizanda anagonjetsa mzinda wa Gaza umene unali likulu la Afilisiti

Malo amene ali pa Mapu

  • GIRISI

  • NYANJA YAIKULU

  • (NYANJA YA MEDITERRANEAN)

  • TURO

  • Sidoni

  • Turo

  • Samariya

  • Yerusalemu

  • Gaza

  • FILISITIYA

  • IGUPUTO

  • BABULO

  • AMONI

  • MOWABU

  • EDOMU

Bwererani ku mutu 7, onani ndime 3

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena