BOKOSI 9C
Yehova Amakwaniritsa Malonjezo Ake—Masiku Ano
1. Kulambira koyera kosaphatikizana ndi kulambira mafano
2. Njala yauzimu inatha
3. Ankapereka nsembe zotamanda Mulungu
4. Anasankha amuna okhulupirika kuti azitsogolera
5. Anthu akulambira Mulungu padziko lonse mogwirizana