Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • rr tsamba 106
  • Maulosi Okhudza Ukapolo ndi Kubwezeretsedwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Maulosi Okhudza Ukapolo ndi Kubwezeretsedwa
  • Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Nkhani Yofanana
  • Mafunso Ochokera kwa Owerenga
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2016
  • “Ndidzawapatsa Mtima Umodzi”
    Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
  • Baibulo ndi Buku la Maulosi Olondola Gawo 2
    Galamukani!—2012
  • Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu
    Nkhani Zina
Onani Zambiri
Yehova Wabwezeretsa Kulambira Koyera
rr tsamba 106

BOKOSI 9D

Maulosi Okhudza Ukapolo Ndi Kubwezeretsedwa

Losindikizidwa

Maulosi ambiri okhudza ukapolo wa Ayuda ku Babulo wakale anakwaniritsidwa m’njira ziwiri. Kukwaniritsidwa kwakukulu kunachitika pamene Akhristu anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo Wamkulu. Onani zitsanzo zotsatirazi.

1. MACHENJEZO

2. UKAPOLO

3. KUBWEZERETSEDWA

KUKWANIRITSIDWA KOYAMBA

Chaka cha 607 B.C.E. chisanafike​—Yesaya, Yeremiya ndi Ezekieli anachenjeza anthu a Mulungu koma anthu ambiri anapitiriza kupandukira Mulungu

607 B.C.E.​—Yerusalemu anawonongedwa, anthu a Mulungu anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo

537 B.C.E. kupita m’tsogolo​—Ayuda okhulupirika amene anatsala anabwerera ku Yerusalemu, anamanga kachisi n’kuyambiranso kulambira koyera

KUKWANIRITSIDWA KWAKUKULU

Nthawi ya atumwi​—Yesu, Paulo ndi Yohane anachenjeza mpingo komabe anthu anapitiriza kupandukira Mulungu

Kuyambira zaka za m’ma 100 C.E.​—Akhristu oona anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo Wamkulu

1919 C.E. kupita m’tsogolo​—Yesu atayamba kulamulira monga mfumu, Akhristu okhulupirika odzozedwa anamasulidwa ku ukapolo wauzimu ndipo kulambira koyera kunabwezeretsedwa

Bwererani ku mutu 9, ndime 6-11, 25-32

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena