Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • w15 3/1 tsamba 7
  • Kodi Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Udzachitika Liti?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Udzachitika Liti?
  • Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
  • Nkhani Yofanana
  • Mwambo Womwe Simuyenera Kuuphonya
    Nsanja ya Olonda—2014
  • “Muzichita Zimenezi Pondikumbukira Ine”
    Utumiki Wathu wa Ufumu—2007
  • Mgonero wa Ambuye uli ndi Tanthauzo Lalikulu kwa Inu
    Nsanja ya Olonda—2003
  • Yehova Amadalitsa Khama Lathu Loyesetsa Kuti Tipezeke pa Chikumbutso
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2023
Onani Zambiri
Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
w15 3/1 tsamba 7
Anthu akuchita mwambo wokumbukira imfa ya Yesu

NKHANI YA PACHIKUTO | YESU ANATIPULUMUTSA KU UCHIMO NDI IMFA

Kodi Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu Udzachitika Liti?

Usiku woti afa mawa lake, Yesu analamula ophunzira ake kuti azichita mwambo wokumbukira imfa yake. Anawauza kuti: “Muzichita zimenezi pondikumbukira.”—Luka 22:19.

Chaka chino, mwambowu udzachitika Lachisanu pa 3 April, dzuwa litalowa. A Mboni za Yehova akukuitanani inuyo limodzi ndi banja lanu kuti mudzabwere kumwambowu. Padzakambidwa nkhani yomwe idzafotokoze kufunika kwa imfa ya Yesu komanso kuti ingakupindulitseni bwanji.

Kuti mudziwe malo ndi nthawi imene mwambowu udzachitike kudera lanu, funsani a Mboni za Yehova a kwanuko kapena pitani pa webusaiti yathu ya www.jw.org/ny.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena