Mawu Oyamba
Kodi ndi madalitso otani amene Mulungu walonjeza anthu? Kodi Mawu ake opezeka m’Malemba Opatulika mungawakhulupirire? Nkhani zotsatirazi zifotokoza madalitso amene Mulungu analonjeza, chifukwa chake muyenera kukhulupirira malonjezowa ndiponso zimene mungachite kuti mudzalandire madalitsowa.