Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb18 November tsamba 4
  • Anapitiriza Kulankhula Mawu a Mulungu Molimba Mtima

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Anapitiriza Kulankhula Mawu a Mulungu Molimba Mtima
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Nkhani Yofanana
  • Yesu Ankakonda Anthu
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • ‘Lankhulani Mawu a Mulungu Molimba Mtima’
    Nsanja ya Olonda—2010
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
mwb18 November tsamba 4
Petulo ndi Yohane akulankhula molimba mtima kwa mkulu wa ansembe ndi anthu ena

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | MACHITIDWE 4-5

Anapitiriza Kulankhula Mawu a Mulungu Molimba Mtima

4:5-13, 18-20, 23-31

Kodi n’chiyani chinathandiza kuti atumwi akhale oyenerera kukhala aphunzitsi? Nanga n’chiyani chinawathandiza kuti azilankhula molimba mtima? Iwo “anali kuyenda ndi Yesu,” yemwe anali Mphunzitsi Wamkulu ndipo anaphunzira kuchokera kwa iye. (Mac. 4:13) Kodi ndi zinthu ziti zimene tikuphunzira kwa Yesu zomwe zingatithandize kuti tikhale aphunzitsi aluso?

Gwirizanitsani malemba otsatirawa ndi maphunziro aperekedwawa.

MALEMBA

PHUNZIRO

  • Mat. 6:33; Maliko 6:31-34

  • Mat. 10:18-20; 21:23-27

  • Mat. 21:15, 16; Yoh. 7:16

  • Mat. 21:22; Luka 22:39-41

  • Tizidalira Yehova

  • Tiziphunzitsa zinthu zochokera m’Malemba

  • Tisamalole kuti anthu ena atichititse mantha

  • Tiziona kuti zinthu za Ufumu ndi zofunika kwambiri kuposa zofuna zathu

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena