Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb19 August tsamba 2
  • “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • “Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • Nkhani Yofanana
  • Timoteo—‘Mwana Weniweni m’Chikhulupiriro’
    Nsanja ya Olonda—1999
  • ‘Sindichititsidwa Manyazi ndi Mbiri Yabwino’
    Nsanja ya Olonda​—1990
  • Kodi N’chiyani Chingatithandize Kulunjika Nawo Bwino Mawu a Choonadi?
    Nsanja ya Olonda—2003
  • ‘Khalani Amphamvu Ndipo Limbikani Mtima’
    Nsanja ya Olonda—2003
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
mwb19 August tsamba 2

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | 2 TIMOTEYO 1-4

“Mulungu Sanatipatse Mzimu Wamantha”

1:7, 8

Timoteyo akuwerenga mpukutu wochokera kwa Paulo

Mawu ouziridwa amene mtumwi Paulo analembera Timoteyo angatipatse mphamvu kuti tizichita zinthu molimba mtima. Sitiyenera kumachita manyazi ndi uthenga wabwino. M’malomwake tiyenera kumalalikira molimba mtima ngakhale zitakhala kuti tikhoza “kumva zowawa.”

Kodi ndiyenera kusonyeza kulimba mtima pa nthawi ziti?

Mtsikana wa Mboni akusonyeza anzake komanso aphunzitsi kabuku kosonyeza mmene moyo unayambira; mlongo akukana kuti amuikire mtengo wa khirisimasi pafupi ndi pomwe amagwirira ntchito; m’bale akulalikira kwa munthu wina yemwe amagwira naye ntchito
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena