Nsembe zanyama zinkaimira nsembe yangwiro ya Yesu
Zimene Tinganene
●○ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu n’chiyani?
Lemba: Mt 6:9, 10 kapena Yes 9:6, 7
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita zotani?
○●ULENDO WOBWEREZA
Funso: Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita zotani?
Lemba: Mt 14:19, 20 kapena Sl 72:16
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi Ufumu wa Mulungu udzayamba liti kulamulira dzikoli?