Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb20 November tsamba 8
  • ‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • ‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
  • Nkhani Yofanana
  • Timathokoza Yehova Chifukwa cha Chikondi Chanu
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2021
  • Yehova Amakonda Munthu Wopereka Mokondwera
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2019
  • “Muzipereka Mphatso kwa Yehova”
    Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2018
  • Kodi Ndingapereke Chiyani kwa Yehova?
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2018
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—Ndandanda ya Misonkhano—2020
mwb20 November tsamba 8
Mkazi wamasiye akuyang’ana tindalama take tiwiri tating’ono asanatipereke.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

‘Timakobidi Tiwiri Tating’ono’ Tamtengo Wapatali

Tindalama timene mayi wamasiye anapereka tinali tochepa kwambiri moti munthu sakanatha kugula nato ngakhale chakudya choti adye kamodzi kokha. (Onani w08 3/1 12 ¶1-3) Koma zimene anaperekazo zinasonyeza kuti ankakonda komanso kulemekeza zimene Yehova wakonza kuti anthu azimulambira. Chifukwa cha zimenezi, chopereka chake chinali chamtengo wapatali kwambiri kwa Atate wake wakumwamba.​—Mko 12:43.

ONERANI VIDIYO YAKUTI ‘MUZIPEREKA MPHATSO KWA YEHOVA,’ KENAKO YANKHANI MAFUNSO OTSATIRAWA:

  • Kachigawo ka m’vidiyo yakuti ‘Muzipereka Mphatso kwa Yehova.’ Zopereka zimagwiritsidwa ntchito pomanga nyumba zothandiza pa zinthu za Ufumu.

    Kodi zopereka zathu zimathandiza pa ntchito monga ziti?

  • Kachigawo ka m’vidiyo yakuti ‘Muzipereka Mphatso kwa Yehova.’ Kamtsikana kakuponya ndalama mu bokosi la zopereka ku Nyumba ya Ufumu.

    N’chifukwa chiyani tinganene kuti zopereka zathu zimakhala zamtengo wapatali ngakhale zikuoneka zochepa?

  • Kachigawo ka m’vidiyo yakuti ‘Muzipereka Mphatso kwa Yehova.’ Zopereka zimathandiza pa ntchito za Ufumu padziko lonse. 1. Ntchito za pa Beteli. 2. Sukulu zophunzitsa atumiki a Mulungu. 3. Ngozi zadzidzidzi. 4. Kumanga nyumba zolambiriramo. 5. Misonkhano ikuluikulu.

    Kodi tingadziwe bwanji zambiri zokhudza mmene tingaperekere ndalama?​—Onani bokosi lakuti “Dziwani Zambiri Pawebusaiti Yathu”

DZIWANI ZAMBIRI PAWEBUSAITI YATHU

Dinani pa mawu oti “Donations” m’munsi mwa tsamba loyamba la pulogalamu ya JW Library. Malinga ndi dziko limene mumakhala, mwina pangakhale linki ina yopita ku nkhani yakuti “Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri” imene imayankha mafunso okhudza zopereka. Vidiyo yakuti Mmene Mungaperekere Zopereka pa Zipangizo za Makono imafotokozanso mfundo zothandiza zokhudza njira zoperekera.

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena