Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb22 November tsamba 7
  • Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa
  • Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Nkhani Yofanana
  • Yoasi Anasiya Kutumikira Yehova Chifukwa Chocheza ndi Anthu Ochita Zoipa
    Nsanja ya Olonda—2009
  • “Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe”​—2Mf 9:8
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
  • Yehoyada Anali Wolimba Mtima
    Zimene Tingaphunzire Munkhani za M’Baibulo
  • Yehova Anachita Zimene Anthu Sankayembekezera
    Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
Onani Zambiri
Kabuku ka Msonkhano wa Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2022
mwb22 November tsamba 7

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Mzimayi Woipa Komanso Wodzimva Analangidwa

Ataliya anapha ana onse achifumu n’cholinga choti iyeyo ayambe kulamulira dziko la Yuda (2Mf 11:1; it-1 209; onani bokosi lakuti “‘Nyumba Yonse ya Ahabu Ifafanizidwe’​—2Mf 9:8”)

Yehoseba anabisa Yehoasi, yemwe anali woyenera kudzakhala mfumu (2Mf 11:2, 3)

Mkulu wa Ansembe Yehoyada anaika Yehoasi kukhala mfumu ndipo anapha Ataliya yemwe anali woipa, ndipo n’kutheka kuti anali womaliza m’nyumba ya Ahabu (2Mf 11:12-16; it-1 209)

FUNSO LOFUNIKA KULIGANIZIRA: Kodi nkhaniyi ikusonyeza bwanji kuti zimene Baibulo limanena pa Miyambo 11:21 ndi pa Mlaliki 8:12, 13 ndi zoona?

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena