Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 July tsamba 13
  • Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Zosankha Zomwe Zimasonyeza Kuti Timadalira Yehova
    Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Kodi Ndingakwanitse Bwanji Zolinga Zanga?
    Galamukani!—2010
  • Khalani ndi Zolinga Zauzimu Kuti Mulemekeze Nazo Mlengi Wanu
    Nsanja ya Olonda—2004
  • Tizivomereza Modzichepetsa Kuti Sitikudziwa Zonse
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova (Yophunzira)—2025
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 July tsamba 13
Njira yokhotakhota yomwe ikuimira kutumikira Yehova. Zikwangwani zomwe zili m’njirayi zikuimira kuphunzira Baibulo, kulalikira, kukhala ndi makhalidwe a Chikhristu komanso luso la kuphunzitsa.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Kodi Muli ndi Zolinga Zotani M’chaka Chautumiki Chikubwerachi?

Zolinga zauzimu zimaphatikizapo chilichonse chimene timayesetsa kuchita kuti tizitumikira Yehova mokwanira komanso tizimusangalatsa. Kukhala ndi zolinga komanso kuzikwaniritsa kumatithandiza kukhala Akhristu olimba mwauzimu ndipo ndi njira yabwino kwambiri imene tingagwiritsire ntchito nthawi ndi mphamvu zathu. (1Ti 4:15) N’chifukwa chiyani tiyenera kumafufuza zolinga zathu nthawi zonse? Chifukwa zochitika pa moyo zimasintha. Cholinga chimene munali nacho poyamba, mwina panopa sichingathekeso kuchikwaniritsa, kapena mwina munachikwaniritsa ndipo mukhoza kuwonjezera china.

Nthawi yabwino yoti mufufuze zolinga zanu ndi pamene chaka chautumiki chatsopano chatsala pang’ono kuyamba. Kodi mungakambirane nkhaniyi pa kulambira kwa pabanja ndi kusankha zolinga zimene mungazikwaniritse panokha kapena limodzi monga banja?

Kodi muli ndi zolinga zotani mu mbali zotsatirazi, nanga mwakonza zotani kuti muzikwaniritse?

Kuwerenga Baibulo, kuphunzira Baibulo panokha, kupezeka pa misonkhano, kuyankha.—w02 6/15 15 ¶14-15

Kulalikira.​—w23.05 27 ¶4-5

Makhalidwe a Chikhristu.​—w22.04 23 ¶5-6

Zina:

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena