Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • mwb23 November tsamba 15
  • N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?
  • Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ndingapewe Bwanji Kuona Zithunzi Zolaula?
    Galamukani!—2007
  • N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula?
    Zimene Achinyamata Amafunsa
  • N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuona Zithunzi Zolaula?
    Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri
  • Kodi Kuonera Zolaula Kuli Ndi Mavuto Otani?
    Nsanja ya Olonda—2013
Onani Zambiri
Utumiki Komanso Moyo Wathu Wachikhristu—2023
mwb23 November tsamba 15

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?

Masiku ano zolaula zili paliponse ndipo zimapezeka mosavuta. Anthu ambiri, ngakhalenso anthu opemphera, amaona kuti kuonera zolaula kulibe vuto lililonse.

Zithunzi za muvidiyo yakuti “Kodi Kuonera Zolaula ndi Tchimo?” 1. Azibambo awiri komanso mzimayi mmodzi ali pa malo okwerera basi ndipo akugwiritsa ntchito mafoni awo. Azibambowo akuona zinthu zolembedwa “XXX.” 2. Kenako bambo mmodzi ali limodzi ndi mkazi wake ndipo akuwerenga nkhani yamutu wakuti “Kodi Baibulo Limaletsa Kuonera Zolaula?” pa jw.org.

ONERANI VIDIYO YAKUTI KODI KUONERA ZOLAULA NDI TCHIMO?, KENAKO YANKHANI FUNSO LOTSATIRALI:

Kodi malemba otsatirawa angatithandize bwanji kumvetsa mmene Mulungu amamvera pa nkhani yoonera zolaula?

  • 1Ak 6:​9, 10

  • Mt 5:28

  • Akl 3:5

  • Yak 1:​14, 15

    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena