Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • yb15 tsamba 10-tsamba 15 ndime 1
  • Zinthu Zikuyenda ku Warwick

Palibe Vidiyo.

Pepani vidiyoyi ikukanika kutsegula.

  • Zinthu Zikuyenda ku Warwick
  • Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015
  • Nkhani Yofanana
  • Kodi Ntchito Yomanga Ikuyenda Bwanji ku Warwick?
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2016
  • Gulu la Yehova Likupita Patsogolo
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova 2014
  • Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi
    Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017
  • Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York
    Nsanja ya Olonda Yolengeza Ufumu wa Yehova—2015
Onani Zambiri
Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2015
yb15 tsamba 10-tsamba 15 ndime 1
Chithunzi chachikulu pamasamba 10, 11

ZIMENE ZACHITIKA M’CHAKA CHAPITACHI

Zinthu Zikuyenda ku Warwick

Chithunzi chachikulu patsamba 12

KU Warwick komwe kukumangidwa likulu lathu latsopano kuli ntchito yaikulu zedi. Abale ndi alongo ambiri akuchita zonse zimene angathe kuti agwire nawo ntchitoyi. Ndipo ambiri akumanena kuti: “Tikuona kuti ndi mwayi wamtengo wapatali kugwira nawo ntchitoyi.” Tamvani mmene ntchitoyi ikuyendera.

Chithunzi patsamba 13

Zimene Anthu Ogwira Ntchito ku Warwick Akunena

Chithunzi patsamba 13

“Kuno ku Warwick kuli ntchito zambiri osati yomanga yokha. Yehova akutithandiza kugwira ntchitoyi mogwirizana kwambiri komanso akutithandiza kudziwa mmene tingapangire mapulani a ntchito zina.”—Enrique Ford.

Chithunzi patsamba 13

“Lemba la Salimo 127:1 limati: ‘Yehova akapanda kumanga nyumba, omanga nyumbayo amagwira ntchito pachabe.’ Mawuwa akutsimikizira kuti Yehova ndi amene angathandize kuti ntchitoyi iyende bwino.”—Troy Snyder.

Chithunzi patsamba 13

“Ntchitoyi yandithandiza kwambiri kulimbitsa chikhulupiriro changa ndipo sindidzaiwala.”—Richard Devine.

Zithunzi pamasamba 14, 15
    Mabuku a Chichewa (1974-2025)
    Tulukani
    Lowani
    • Chichewa
    • Tumizirani Ena
    • Zimene Mumakonda
    • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
    • Zoyenera Kutsatira
    • Nkhani Yosunga Chinsinsi
    • Privacy Settings
    • JW.ORG
    • Lowani
    Tumizirani Ena