Genesis 35:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli+ ukakhale kumeneko. Ukandimangire guwa lansembe. Ndine Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unkathawa mchimwene wako Esau.”+
35 Zitatero, Mulungu anauza Yakobo kuti: “Nyamuka, pita ku Beteli+ ukakhale kumeneko. Ukandimangire guwa lansembe. Ndine Mulungu woona, amene anaonekera kwa iwe pamene unkathawa mchimwene wako Esau.”+