Genesis 35:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukatero, tinyamuke tipite ku Beteli. Kumeneko ndikamangira guwa lansembe Mulungu woona, amene anandiyankha pa tsiku la kusautsika kwanga, ndipo wakhala nane kulikonse kumene ndapita.”+
3 Mukatero, tinyamuke tipite ku Beteli. Kumeneko ndikamangira guwa lansembe Mulungu woona, amene anandiyankha pa tsiku la kusautsika kwanga, ndipo wakhala nane kulikonse kumene ndapita.”+