Genesis 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ana a Reueli, mwana wamwamuna wa Esau ndi awa: Mfumu Nahati, Mfumu Zera, Mfumu Shama ndi Mfumu Miza. Amenewa ndi amene anali mafumu akubanja la Reueli mʼdziko la Edomu.+ Amenewa anali ana a Basemati mkazi wa Esau.
17 Ana a Reueli, mwana wamwamuna wa Esau ndi awa: Mfumu Nahati, Mfumu Zera, Mfumu Shama ndi Mfumu Miza. Amenewa ndi amene anali mafumu akubanja la Reueli mʼdziko la Edomu.+ Amenewa anali ana a Basemati mkazi wa Esau.