Genesis 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iyi ndi mbiri ya Yakobo. Yosefe+ ali ndi zaka 17, anapita kokadyetsa nkhosa+ limodzi ndi ana a Biliha+ ndi ana a Zilipa,+ omwe anali akazi a bambo ake. Ndiyeno Yosefe anakauza bambo ake zoipa zimene abale akewo ankachita. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 37:2 Nsanja ya Olonda,8/1/2014, tsa. 115/1/1987, tsa. 12 Galamukani!,9/8/1988, ptsa. 16-17
2 Iyi ndi mbiri ya Yakobo. Yosefe+ ali ndi zaka 17, anapita kokadyetsa nkhosa+ limodzi ndi ana a Biliha+ ndi ana a Zilipa,+ omwe anali akazi a bambo ake. Ndiyeno Yosefe anakauza bambo ake zoipa zimene abale akewo ankachita.