Genesis 37:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Abale akewo anamufunsa kuti: “Kodi zoona iweyo ukuganiza kuti ungadzakhale mfumu yathu nʼkumatilamulira?”+ Choncho maloto amenewa komanso zimene ananena zinapangitsa kuti abale akewo apeze chifukwa chinanso choti azidana naye.
8 Abale akewo anamufunsa kuti: “Kodi zoona iweyo ukuganiza kuti ungadzakhale mfumu yathu nʼkumatilamulira?”+ Choncho maloto amenewa komanso zimene ananena zinapangitsa kuti abale akewo apeze chifukwa chinanso choti azidana naye.