Genesis 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho dziko lapansi linayamba kumera udzu, zomera zobereka mbewu+ monga mwa mitundu yake komanso mitengo yobereka zipatso zokhala ndi nthangala monga mwa mitundu yake. Zitatero, Mulungu anaona kuti zili bwino. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:12 Galamukani!,3/2014, tsa. 7
12 Choncho dziko lapansi linayamba kumera udzu, zomera zobereka mbewu+ monga mwa mitundu yake komanso mitengo yobereka zipatso zokhala ndi nthangala monga mwa mitundu yake. Zitatero, Mulungu anaona kuti zili bwino.