Genesis 37:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Rubeni anawauza kuti: “Musakhetse magazi.+ Muponyeni mʼchitsime chopanda madzichi kutchire kuno, koma musamuvulaze.”+ Cholinga chake chinali chakuti amupulumutse kwa iwo nʼkumubwezera kwa bambo ake.
22 Rubeni anawauza kuti: “Musakhetse magazi.+ Muponyeni mʼchitsime chopanda madzichi kutchire kuno, koma musamuvulaze.”+ Cholinga chake chinali chakuti amupulumutse kwa iwo nʼkumubwezera kwa bambo ake.