-
Genesis 38:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Atagona naye, mkaziyo ananyamuka nʼkubwerera kwawo. Atafika anavula nsalu imene anadziphimba nayo ija nʼkuvala zovala zake zaumasiye.
-