-
Genesis 38:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Choncho Yuda anati: “Mulekeni atenge zinthuzo zikhale zake, kuopera kuti anthu angatiseke. Ndipotu mwana wa mbuziyo ndinatumiza ndithu, koma mkaziyo sunakamupeze.”
-