Genesis 38:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno Yuda atayangʼanitsitsa zinthuzo, ananena kuti: “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine, chifukwa sindinamupereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagonenso naye. Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 38:26 Nsanja ya Olonda,1/15/2004, tsa. 29
26 Ndiyeno Yuda atayangʼanitsitsa zinthuzo, ananena kuti: “Mkaziyu ndi wolungama koposa ine, chifukwa sindinamupereke kwa mwana wanga Shela.”+ Zitatero, Yuda sanagonenso naye.