-
Genesis 40:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Mkulu wa ophika mkate ataona kuti Yosefe wamasulira zabwino, nayenso anati: “Inenso ndinalota maloto. Ndinalota nditasenza pamutu pangapa mabasiketi atatu a mikate yoyera.
-