Genesis 41:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inuyo Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu. Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera mʼndende yakunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+
10 Inuyo Farao munatikwiyira kwambiri ife atumiki anu. Ineyo ndi mkulu wa ophika mkate munatitsekera mʼndende yakunyumba kwa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+