Genesis 41:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kundendeko tonse awiri tinalota maloto usiku umodzi. Aliyense analota maloto ndipo malotowo anali ndi matanthauzo osiyana.+
11 Kundendeko tonse awiri tinalota maloto usiku umodzi. Aliyense analota maloto ndipo malotowo anali ndi matanthauzo osiyana.+