Genesis 41:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tinalinso ndi mnyamata wina wa Chiheberi kumeneko. Iyeyo anali wantchito wa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Titamufotokozera maloto athu,+ anatimasulira matanthauzo ake. Aliyense anamumasulira mogwirizana ndi maloto amene analota.
12 Tinalinso ndi mnyamata wina wa Chiheberi kumeneko. Iyeyo anali wantchito wa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Titamufotokozera maloto athu,+ anatimasulira matanthauzo ake. Aliyense anamumasulira mogwirizana ndi maloto amene analota.