Genesis 41:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yosefe anayankha Farao kuti: “Mulungu ndi amene anene nkhani yabwino yokhudza inu Farao, osati ine.”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 41:16 Nsanja ya Olonda,2/1/2015, ptsa. 14-15
16 Yosefe anayankha Farao kuti: “Mulungu ndi amene anene nkhani yabwino yokhudza inu Farao, osati ine.”+