Genesis 41:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Njala ija inapitirizabe padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo nʼkuyamba kugulitsa chakudya kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri mʼdziko la Iguputo.
56 Njala ija inapitirizabe padziko lonse lapansi.+ Zitatero, Yosefe anayamba kutsegula nkhokwe zonse zimene zinali pakati pawo nʼkuyamba kugulitsa chakudya kwa Aiguputo,+ chifukwa njalayo inali itafika poipa kwambiri mʼdziko la Iguputo.