Genesis 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yakobo sanalole kuti Benjamini,+ mʼbale wake wa Yosefe, apite limodzi ndi abale akewo chifukwa anati: “Mwina ngozi yoopsa ingamuchitikire nʼkufa.”+
4 Koma Yakobo sanalole kuti Benjamini,+ mʼbale wake wa Yosefe, apite limodzi ndi abale akewo chifukwa anati: “Mwina ngozi yoopsa ingamuchitikire nʼkufa.”+