Genesis 42:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yosefe ndi amene anali wolamulira mʼdzikomo+ ndipo ndi amene ankagulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye ndipo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 42:6 Nsanja ya Olonda,5/1/2015, tsa. 13
6 Yosefe ndi amene anali wolamulira mʼdzikomo+ ndipo ndi amene ankagulitsa tirigu kwa anthu onse ochokera kumayiko ena onse.+ Choncho abale a Yosefe anafika kwa iye ndipo anagwada nʼkumuweramira mpaka nkhope zawo pansi.+