-
Genesis 42:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Atatero Yosefe analamula anyamata ake kuti awathirire tirigu mʼmatumba awo mpaka kudzaza komanso kuti aliyense amubwezere ndalama zake pomuikira mʼthumba lake. Anawalamulanso kuti awapatse chakudya cha pa ulendo. Anyamatawo anawachitiradi zimenezo.
-