-
Genesis 42:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Atafika pamalo oti agone, mmodzi wa iwo anamasula thumba lake kuti atengemo chakudya choti apatse bulu wake. Atamasula, anangoona kuti ndalama zake zili pakamwa pa thumbalo.
-