Genesis 42:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndiye nduna yaikulu ya dzikolo inatiuza kuti, ‘Ngati mulidi achilungamo muchite izi: Mmodzi wa inu atsale ndi ine kuno.+ Koma enanu tengani chakudya, mupite nacho kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+
33 Ndiye nduna yaikulu ya dzikolo inatiuza kuti, ‘Ngati mulidi achilungamo muchite izi: Mmodzi wa inu atsale ndi ine kuno.+ Koma enanu tengani chakudya, mupite nacho kunyumba zanu chifukwa kuli njala.+