Genesis 42:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Yakobo bambo awo anadandaula kuti: “Inetu mwandisandutsa namfedwa!+ Yosefe anapita,+ Simiyoni kulibenso.+ Tsopano mukufuna kutenga Benjamini! Nʼchifukwa chiyani zonsezi zikundichitikira?”
36 Yakobo bambo awo anadandaula kuti: “Inetu mwandisandutsa namfedwa!+ Yosefe anapita,+ Simiyoni kulibenso.+ Tsopano mukufuna kutenga Benjamini! Nʼchifukwa chiyani zonsezi zikundichitikira?”