Genesis 43:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tirigu amene anabweretsa kuchokera ku Iguputo+ uja atatha, bambo awo anawauza kuti: “Pitaninso mukatigulireko kachakudya pangʼono.”
2 Tirigu amene anabweretsa kuchokera ku Iguputo+ uja atatha, bambo awo anawauza kuti: “Pitaninso mukatigulireko kachakudya pangʼono.”